Ndondomeko zofunikira za ulimi oyenera - Za alimi ang'onoang'ono a tiyi Kuteteza mbewu ku tizilombo (kuthana ndi matenda wotchedwa Armilaria owononga mitengo ya tiyi)
Mtengo wa tiyi wang'aluka ndipo ukutulutsa tiufa toyera
Zulani phata lonse ndi mizu yomwe ndipo mutenthe
Kuteteza mbewu ku tizilombo (kutengulira)
Kasamalidwe ka zinyalala zomwe zimatha kuwola
Kupanga manyowa kuchokela ku zinyalala zomwe zimatha kuwola